Zekariya 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndadzikokera Yuda, ndadzaza uta ndi Efraimu; ndipo ndidzautsa ana ako, Ziyoni, alimbane nao ana ako, Yavani, ndipo ndidzakuyesa lupanga la ngwazi.

Zekariya 9

Zekariya 9:10-17