Zekariya 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu: Cikakhala codabwitsa pamaso pa otsala a anthu awa masiku awo, kodi cidzakhalanso codabwitsa pamaso panga? ati Yehova wa makamu.

Zekariya 8

Zekariya 8:3-16