Zekariya 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo musalingirira coipa m'mtima mwanu yense pa mnzace; nimusakonde lumbiro lonama; pakuti izi zonse ndidana nazo, ati Yehova.

Zekariya 8

Zekariya 8:8-23