Zekariya 8:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Yehova wa makamu: Monga ndil nalingirira kucitira inu coipa, muja makolo anu anautsa mkwiyo wanga, ati Yehova wa makamu, ndipo sindinawaleka;

Zekariya 8

Zekariya 8:9-22