Zekariya 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanene kwa ansembe a nyumba ya Yehova wa makamu, ndi kwa aneneri, ndi kuti, Kodi ndilire mwezi wacisanu, ndi kudzipatula, monga umo ndikacitira zaka izi zambiri?

Zekariya 7

Zekariya 7:1-4