Zekariya 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma ndidzawabalalitsa ndi kabvumvulu mwa amitundu onse amene sanawadziwa. Motero dziko linakhala bwinja, m'mbuyo mwao; palibe munthu wopitapo ndi kubwererako; pakuti adaika dziko lofunikalo labwinja.

Zekariya 7

Zekariya 7:10-14