Zekariya 5:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa ine, Ili ndi temberero lirikuturukira pa dziko lonse; pakuti ali yense wakuba adzapitikitsidwa kuno monga mwa ili; ndi ali yense wakulumbira zonama adzapitikitsidwa kuno monga mwa ili.

Zekariya 5

Zekariya 5:1-9