Zekariya 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiwe yani, phiri lalikuru iwe? pamaso pa Zerubabele udzasanduka cidikha; ndipo adzaturutsa mwala wa cimbudzi, ndi kupfuula, Cisomo, cisomo nao.

Zekariya 4

Zekariya 4:1-13