Zekariya 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tamvera tsono, Yoswa mkulu wa ansembe, iwe ndi anzako akukhala pansi pamaso pako; pakuti iwo ndiwo cizindikilo; pakuti taonani, ndidzafikitsa mtumiki wanga, ndiye Mphukira.

Zekariya 3

Zekariya 3:6-10