Zekariya 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anayankha nanena ndi iwo akuima pamaso pace, ndi kuti, Mumbvule nsaru zonyansazi. Nati kwa iye, Taona, ndakucotsera mphulupulu zako, ndipo ndidzakubveka: zobvala za mtengo wace.

Zekariya 3

Zekariya 3:2-9