Zekariya 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anandionetsa Yoswa mkulu wa ansembe alikuima pamaso pa mthenga wa Yehova, ndi Satana alikuima pa dzanja lace lamanja, atsutsana naye.

Zekariya 3

Zekariya 3:1-4