Zekariya 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, taonani, ndidzawayambasira dzanja langa, ndipo adzakhala zofunkha za iwo amene anawatumikira; ndipo mudzadziwa kuti Yehova wa makamu anandituma.

Zekariya 2

Zekariya 2:7-12