Zekariya 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amitundu ambiri adzaphatikidwa kwa Yehova tsiku ilo, nadzakhala anthu anga; ndipo ndidzakhala pakati pako, ndipo udzadziwa kuti Yehova wa makamu anandituma kwa iwe.

Zekariya 2

Zekariya 2:8-13