Zekariya 14:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo padzaoneka pa miriu ya akavalo OPATULIKIRA YEHOVA; ndi mbiya za m'nyumba ya Yehova zidzanga mbale za ku guwa la nsembe.

Zekariya 14

Zekariya 14:12-21