Zekariya 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Galamuka, lupanga, pa mbusa wanga, ndi pa munthu mnzanga wa pamtima, ati Yehova wa makamu; kantha mbusa, ndi nkhosa zidzabalalika; koma ndidzabwezera dzanja langa pa zazing'onozo.

Zekariya 13

Zekariya 13:2-9