Zekariya 12:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika tsiku ilo, ndidzaika Yerusalemu akhale mwala wolemetsa mitundu yonse ya anthu; onse akuusenza adzadzilasa nao; ndi amitundu onse a pa dziko lapansi adzasonkhana kutsutsana nao.

Zekariya 12

Zekariya 12:1-4