Zekariya 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katundu wa mau a Yehova wakunena Israyeli.Atero Yehova, wakuyala miyamba, ndi kuika maziko a dziko lapansi, ndi kulenga mzimu wa munthu m'kati mwace;

Zekariya 12

Zekariya 12:1-8