Zekariya 11:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cema, mtengo wamlombwa, pakuti mkungudza wagwa, popeza mitengo yokoma yaipitsidwa; cemani athundu a ku Basani, pakuti nkhalango yocinjirizika yagwa pansi.

Zekariya 11

Zekariya 11:1-5