Zekariya 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo a ku Efraimu adzakhala ngati ngwazi, ndi mtima wao udzakondwera ngati ndi vinyo; ndipo ana ao adzaciona nadzakondwera; mtima wao udzakondwerera mwa Yehova.

Zekariya 10

Zekariya 10:1-11