Zekariya 10:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakhala ngati ngwazi zakupondereza adani m'thope la kubwalo kunkhondo; ndipo adzacita nkhondo, cifukwa Yehova ali nao; ndi apakavalo adzacitidwa manyazi.

Zekariya 10

Zekariya 10:1-9