Zekariya 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace uziti nao, Atero Yehova wa makamu: Bwererani kudza kwa Ine, ati Yehova wa makamu, ndipo Ine ndidzabwerera kudza kwa inu, ati Yehova wa makamu.

Zekariya 1

Zekariya 1:1-7