Zekariya 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinati kwa mthenga wakulankhula ndi ine, Izi nziani? Ndipo anandiyankha, Izi ndi nyangazi zinabalalitsa Yuda, Israyeli, ndi Yerusalemu.

Zekariya 1

Zekariya 1:18-21