Zekariya 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova: Ndabwera kudza ku Yerusalemu ndi zacifundo; nyumba yanga idzamangidwamo, ndipo adzayesa Yerusalemu ndi cingwe.

Zekariya 1

Zekariya 1:15-21