Zekariya 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wakulankhula ndi ine anati kwa ine, Pfuula, ndi kuti, Atero Yehova wa makamu: Ndicitira nsanje Yerusalemu ndi Ziyoni ndi nsanje yaikuru.

Zekariya 1

Zekariya 1:11-21