Zekariya 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wa Yehova anayankha nati, Yehova wa makamu, mudzakhala mpaka liti osacitira cifundo Yerusalemu, ndi midzi ya Yuda, imene munakwiya nayo zaka izi makumi asanu ndi awiri?

Zekariya 1

Zekariya 1:4-17