Zefaniya 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova Mulungu wako ali pakati pako, wamphamvu wakupulumutsa; adzakondwera nawe ndi cimwemwe, adzakhala wopanda thamo m'cikondi cace; adzasekerera nawe ndi kuyimbirapo.

Zefaniya 3

Zefaniya 3:16-20