Zefaniya 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uwu ndi mudzi wosekererawo unakhala wosasamalira, unanena m'mtima mwace, Ine ndine, ndi wopanda ine palibe wina; ha! wasanduka bwinja, mogonera nyama za kuthengo! yense wakuupitirira adzatsonya mtsonyo, ndi kupukusa mutu.

Zefaniya 2

Zefaniya 2:12-15