Zefaniya 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zolemera zao zidzakhala zakufunkhidwa; ndi nyumba zao zabwinja; adzamangadi nyumba, koma sadzagonamo; adzanka minda yampesa koma sadzamwa vinyo wace.

Zefaniya 1

Zefaniya 1:8-18