Yuda 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mikayeli mkulu wa angelo, pakucita makani ndi mdierekezi anatsutsana za thupi la Mose, sanalimbika mtima kumehulira cifukwa comcitira mwano, koma anati, Ambuye akudzudzule.

Yuda 1

Yuda 1:4-13