Yoweli 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzagulitsa ana ako amuna ndi akazi m'dzanja la ana a Yuda; ndipo iwo adzawagulitsa kwa anthu a Seba, kwa anthu okhala kutari; pakuti Yehova wanena.

Yoweli 3

Yoweli 3:3-9