Yoweli 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atumphako ngati mkokomo wa magareta pamwamba pa mapiri, ngati kulilima kwa malawi a moto akupsereza ziputu, ngati mtundu wamphamvu wa anthu ondandalikira nkhondo.

Yoweli 2

Yoweli 2:1-7