Yoweli 2:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika m'tsogolo mwace, ndidzatsanulira mzimu wanga pa anthu onse, ndi ana anu amuna ndi akazi adzanenera, akulu akulu anu adzalota maloto, anyamata anu adzaona masomphenya;

Yoweli 2

Yoweli 2:18-31