Yoweli 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kaya, kapena adzabwerera, nadzalekerera, ndi kusiya mdalitso pambuyo pace, ndiwo nsembe yaufa ndi nsembe yathira ya Yehova Mulungu wanu.

Yoweli 2

Yoweli 2:10-18