Yoweli 1:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. MAU a Yehova a kwa Yoeli mwana wa Petueli.

2. Imvani ici, akulu akulu inu, nimuchere khutu, inu nonse okhala m'dziko. Cacitika ici masiku anu kodi, kapena masiku a makolo anu?

3. Mufotokozere ana anu ici, ndi ana anu afotokozere ana ao, ndi ana ao afotokozere mbadwo wina.

Yoweli 1