Yoswa 9:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku lija Yoswa anawasandutsa akutema nkhuni, ndi otungira madzi msonkhanowo, ndi guwa la nsembe la Yehova, mpaka lero lino, pamalopo akadzasankha.

Yoswa 9

Yoswa 9:21-27