Yoswa 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuru athu ndi nzika zonse za m'dziko mwathu zidanena nafe ndi kuti, Mutenge m'dzanja lanu kamba wa paulendo, kakomane naoni, nimunene nao, Ndife akapolo anu; ndipo tsopano mupangane nafe.

Yoswa 9

Yoswa 9:9-15