Yoswa 7:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amuna a ku Ai anawakantha amuna, ngati makumi atatu mphambu asanu ndi mmodzi; nawapitikitsa kuyambira pacipata mpaka ku Sebarimu, nawakantha potsika; ndi mitima ya anthu inasungunuka inga madzi.

Yoswa 7

Yoswa 7:1-13