Yoswa 7:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuuniikira mulu waukuru wamiyala, wokhalako kufikira lero lino; ndipo Yehova anatembenuka kusiya mkwiyo wace waukuru. Cifukwa cace anacha dzina lace la malowo, Cigwa ca Akori, mpaka lero lino.

Yoswa 7

Yoswa 7:25-26