Yoswa 7:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yoswa anatuma mithenga, iwo nathamangira kuhema; ndipo taonani, zidabisika m'hema mwace ndi siliva pansi pace.

Yoswa 7

Yoswa 7:20-26