Yoswa 7:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anati kwa Akani, Mwana wanga, ucitiretu ulemu Yehova Mulungu wa Israyeli, numlemekeze iye; nundiuze tsopano, wacitanji? usandibisire.

Yoswa 7

Yoswa 7:15-20