Yoswa 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa ananena kwa amuna awiri anazonda dzikowo, Lowani m'nyumba ya mkazi wadamayo, ndi kuturutsamo mkaziyo ndi zonse ali nazo, monga munamlumbirira iye.

Yoswa 6

Yoswa 6:13-24