Yoswa 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa analamulira anthu, ndi kuti, Musamapfuula, kapena kumveketsa mau anu, asaturuke konse mau m'kamwa mwanu, mpaka tsiku lakunena nanu ine, Pfuulani; pamenepo muzipfuula.

Yoswa 6

Yoswa 6:3-20