Yoswa 4:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena nao Yoswa, Olokani, kutsogolera likasa la Yehova Mulungu wanu pakati pa Yordano, nimudzisenzere yense mwala paphewa pace, monga mwa kuwerenga kwa mapfuko a ana a Israyeli;

Yoswa 4

Yoswa 4:1-8