Yoswa 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo muwalamulire iwo ndi kuti, Mudzitengere pano pakati pa Yordano, poimapo mapazi a ansembe, miyala khumi ndi iwiri, ndi kuoloka nayo, ndi kulika m'mogona m'mene mugonamo usiku uno.

Yoswa 4

Yoswa 4:1-7