Yoswa 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anakwera kuturuka m'Yordano tsiku lakhumi la mwezi woyamba, namanga misasa ku Giligala, mbali ya ku m'mawa kwa Yeriko.

Yoswa 4

Yoswa 4:11-24