Yoswa 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ansembe akusenza likasa anaima pakati pa Yordano, mpaka zitatha zonse Yehova adazilamulira Yoswa anene kwa anthu, monga mwa zonse Mose adalamulira Yoswa; ndipo anthu anafulumira kuoloka.

Yoswa 4

Yoswa 4:2-12