Yoswa 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe akulisenza likasa la cipangano la Yehova, anaima pouma pakati pa Yordano, ndi Aisrayeli onse anaoloka pouma mpaka mtundu wonse unatha kuoloka Yordano.

Yoswa 3

Yoswa 3:15-17