Yoswa 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa analawirira mamawa, kucoka ku Sitimu, nafika ku Yordano, iye ndi ana onse a Israyeli; nagona komweko, asanaoloke.

Yoswa 3

Yoswa 3:1-4