Yoswa 24:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Israyeli anatumikira Yehova masiku onse a Yoswa, ndi masiku onse a akulu akulu otsala atafa Yoswa, amene anadziwa nchito yonse ya Yehova anaicitira Israyeli.

Yoswa 24

Yoswa 24:24-33