Yoswa 24:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anati kwa anthu onse, Taonani, mwala uwu udzakhala mboni yotitsutsa; pakuti udamva mau onse a Yehova amene ananena kwa ife; ndipo udzakhala mboni yotsutsa inu, mungakanize Mulungu wanu.

Yoswa 24

Yoswa 24:22-33